Chichewa Devotion


27
May 2019
Dalirani Mawu Ake - Mtumwi Joseph Ziba

MBEWU ZA CHIPAMBANO – Lolemba, 27 May 2019 DALIRANI MAWU AKE – Mtumwi Joseph Ziba “momwemo adzakhala mau anga amene atuluka m’kamwa mwanga, sadzabwerera kwa Ine chabe, koma adzachita chimene ndifuna, ndipo adzakula m’mene ndinawatumizira.” Yesaya 55:11 (Buku lopatulika) Cholakwika chachikulu chimene mungapange ndi ku taya mtima ndi Mulungu, ndi kuganiza kuti mawu ake sangakusintheni. Mutha kukhala kuti mukudutsa mu nyengo zowawitsa, ndipo zinthu sizikuyenda Mnyengo zina. Ngakhale zili choncho phunzirani kudalira mawu a Mulungu mu nyengo ngati zimenezi. Vesi lili pamwambalo likuti mawu a Mulungu adzachita chimene atumidwira, sadzabwerera kwa Iye chabe. Amapeleka......

Read More