Tag: Financial Summit


24
Dec 2018
Chisankho n’chanu kukhala moyo wochita bwino - Apostle Joseph Ziba

MBEWU ZACHIPAMBANO – Lolemba, 24 December, 2018 Chisankho n’chanu kukhala moyo wochita bwino Ndi M’tumwi Joseph Ziba Buku ili la chilamulo lisachoke pakamwa pako; koma ulingiriremo usana ndi usiku, kuti usamalire kuchita monga mwa zonse zolembedwamo; popeza ukatero udzakometsa njira yako, nudzachita mwanzeru. Yoswa 1: 8 KJV Tsiku lina, posinkhasinkha ndi kullingalira Mawu a Mulungu, Atate adanditsegula maso ku mfundo zomwe zimapangitsa munthu kupambana mwaumulungu m’moyo uno. Pamene ndinkangokhalira kukondwera ndikudziviika mu zomwe Atate amavumbulutsa, Iye anandifusa funso lomwe limaoneka ngati “losamvetsetseka.’ Iye anati: “Mwana wanga, Kodi umaganiza kuti n’chifukwa chiyani ndidayikiza mfundo zokhudzana ndi......

Read MoreApril 27, 2018

Why Rising on Top?

  WHY RISING ON TOP  Some people have been asking me why we call these meetings “Rising On Top” instead of “Rising to the Top”. They feel like naming these meetings “Rising to the Top”...